Salimo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma oipa sali choncho.Iwo ali ngati mankhusu* amene amauluzika ndi mphepo.+ Yesaya 30:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ng’ombe ndi abulu akuluakulu olima, zidzadya chakudya chokoma chosakaniza ndi zitsamba zowawasira, chimene mankhusu ake anauluzidwa pogwiritsa ntchito fosholo+ ndi chifoloko.
24 Ng’ombe ndi abulu akuluakulu olima, zidzadya chakudya chokoma chosakaniza ndi zitsamba zowawasira, chimene mankhusu ake anauluzidwa pogwiritsa ntchito fosholo+ ndi chifoloko.