Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Chidzakhala chotembereredwa chipatso cha mimba yako,+ chipatso cha nthaka yako,+ ana a ng’ombe zako ndi ana a nkhosa zako.+

  • Yeremiya 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+

  • Ezekieli 24:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 ‘Uza nyumba ya Isiraeli kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndidetsa malo anga opatulika,+ chinthu chimene mumachinyadira kwambiri,+ chinthu chosiririka kwa inu,+ ndiponso chinthu chimene mumachichitira chifundo. Ana anu aamuna ndi aakazi amene munawasiya m’mbuyo adzaphedwa ndi lupanga.+

  • Hoseya 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pakuti ngakhale alere ana awo, ine ndidzawaphera anawo moti sadzakula n’kukhala amuna.+ Tsoka kwa iwo ndikadzawachokera!+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena