Deuteronomo 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana anu adzakhala otembereredwa*+ komanso chipatso cha nthaka yanu, ana a ngʼombe zanu ndi ana a nkhosa zanu adzakhala otembereredwa.+
18 Ana anu adzakhala otembereredwa*+ komanso chipatso cha nthaka yanu, ana a ngʼombe zanu ndi ana a nkhosa zanu adzakhala otembereredwa.+