Salimo 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi palibe aliyense wozindikira mwa anthu ochita zopweteka anzawowa,+Amene akudya anthu anga ngati chakudya?+Iwo sanaitane pa Yehova.+ Amosi 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova wanena kuti, ‘Popeza kuti Isiraeli anapanduka mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anagulitsa munthu wolungama kuti apeze siliva komanso anagulitsa munthu wosauka pa mtengo wa nsapato.+
4 Kodi palibe aliyense wozindikira mwa anthu ochita zopweteka anzawowa,+Amene akudya anthu anga ngati chakudya?+Iwo sanaitane pa Yehova.+
6 “Yehova wanena kuti, ‘Popeza kuti Isiraeli anapanduka mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anagulitsa munthu wolungama kuti apeze siliva komanso anagulitsa munthu wosauka pa mtengo wa nsapato.+