Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Usapotoze chigamulo cha munthu wosauka wokhala pakati panu, pa mlandu wake.+

  • Ezekieli 22:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anthu alandira ziphuphu kuti akhetse magazi.+ Iwe walandira chiwongoladzanja+ ndi kuchita katapira.+ Ukupeza phindu losayenera mwa kubera anzako+ mwachinyengo+ ndipo ine wandiiwala,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

  • Yoweli 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mitunduyi inali kuchitira maere anthu anga+ ndipo inali kupereka mwana wamwamuna kuti akhale malipiro a hule.+ Inali kupereka mwana wamkazi kuti akhale malipiro a vinyo woti amwe.

  • Amosi 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Inu mukulamula anthu osauka kuti akulipireni mwa kukupatsani zokolola zawo za m’munda, ndiponso kuti azikhoma msonkho mwa kupereka mbewu za m’munda.+ Choncho chifukwa mwachita zinthu zimenezi, simudzapitiriza kukhala m’nyumba zamiyala yosema zimene mwamanga+ ndipo simudzamwa vinyo wochokera m’minda yanu ya mpesa yosiririkayo.+

  • Amosi 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kodi sabata litha liti kuti tigule anthu onyozeka ndi ndalama zasiliva, kuti tigule munthu wosauka pa mtengo wa nsapato ndiponso kuti tigulitse mbewu zachabechabe?’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena