Deuteronomo 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munaiwala Thanthwe limene linakuberekani,+Ndipo munayamba kuiwala Mulungu amene anachititsa kuti mukhalepo kudzera mwa zowawa za pobereka.+ Salimo 106:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo anaiwala Mulungu, Mpulumutsi wawo,+Amene anachita zinthu zazikulu ku Iguputo,+
18 Munaiwala Thanthwe limene linakuberekani,+Ndipo munayamba kuiwala Mulungu amene anachititsa kuti mukhalepo kudzera mwa zowawa za pobereka.+