Yesaya 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Nyumba za njerwa n’zimene zagwazi, koma ife timanga zina za miyala yosema.+ Mitengo ya mkuyu ndi imene yathyoledwayi, koma m’malo mwake ife tipezerapo mitengo ya mkungudza.”+ Zefaniya 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chuma chawo chidzafunkhidwa ndipo nyumba zawo zidzakhala bwinja.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.+ Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wochokera mmenemo.+
10 “Nyumba za njerwa n’zimene zagwazi, koma ife timanga zina za miyala yosema.+ Mitengo ya mkuyu ndi imene yathyoledwayi, koma m’malo mwake ife tipezerapo mitengo ya mkungudza.”+
13 Chuma chawo chidzafunkhidwa ndipo nyumba zawo zidzakhala bwinja.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.+ Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wochokera mmenemo.+