Ekisodo 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ukabwereketsa ndalama kwa anthu anga, kwa munthu wovutika amene ali pafupi ndi iwe,+ usakhale ngati munthu wopereka ngongole yakatapira* kwa iye. Usafunepo chiwongoladzanja.+ Deuteronomo 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “M’bale wako usamulipiritse chiwongoladzanja+ pa ndalama, chakudya+ kapena chilichonse chimene munthu angafunepo chiwongoladzanja.
25 “Ukabwereketsa ndalama kwa anthu anga, kwa munthu wovutika amene ali pafupi ndi iwe,+ usakhale ngati munthu wopereka ngongole yakatapira* kwa iye. Usafunepo chiwongoladzanja.+
19 “M’bale wako usamulipiritse chiwongoladzanja+ pa ndalama, chakudya+ kapena chilichonse chimene munthu angafunepo chiwongoladzanja.