Levitiko 25:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Musam’kongoze ndalama kuti adzabweze chiwongoladzanja,+ ndipo musakongoze chakudya chanu mwa kuchititsa katapira.
37 Musam’kongoze ndalama kuti adzabweze chiwongoladzanja,+ ndipo musakongoze chakudya chanu mwa kuchititsa katapira.