Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 23:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mlendo+ ungamulipiritse chiwongoladzanja, koma m’bale wako usamulipiritse chiwongoladzanja,+ kuti Yehova Mulungu wako akudalitse pa zochita zako zonse m’dziko limene ukupita kukalitenga kukhala lako.+

  • Nehemiya 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiponso ine, abale anga ndi atumiki anga, tikukongoza ndalama ndi chakudya kwa abale athu. Chonde, tiyeni tileke kulandira chiwongoladzanja tikakongoza zinthu.+

  • Luka 6:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Mosiyana ndi zimenezo, inu pitirizani kukonda adani anu. Pitirizani kuchita zabwino, ndi kukongoza+ popanda chiwongoladzanja, osayembekezera kulandira kalikonse. Mukatero, mphoto yanu idzakhala yaikulu ndipo mudzakhala ana a Wam’mwambamwamba,+ chifukwa iye ndi wachifundo+ kwa osayamika ndi kwa oipa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena