Nehemiya 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho ndinayamba kuganiza mumtima mwanga ndipo ndinapeza kuti anthu olemekezeka ndi atsogoleri anali olakwa.+ Pamenepo ndinawauza kuti: “Nonsenu mukuumiriza abale anu kukupatsani chiwongoladzanja chokwera kwambiri.”+ Kenako ndinaitanitsa msonkhano waukulu chifukwa cha iwowa.+ Ezekieli 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ngati salandira chiwongoladzanja akabwereketsa zinthu,+ ndiponso sakongoza zinthu mwa katapira,*+ ngati sachita zopanda chilungamo,+ ngati amachita chilungamo chenicheni poweruza munthu ndi mnzake,+ Ezekieli 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye amakongoza zinthu zake mwa katapira+ ndipo amalandira chiwongoladzanja.+ Ndithudi iye sadzakhala ndi moyo chifukwa wachita zinthu zonyansa zonsezi.+ Adzaphedwa ndithu, ndipo magazi ake adzakhala pamutu pake.+
7 Choncho ndinayamba kuganiza mumtima mwanga ndipo ndinapeza kuti anthu olemekezeka ndi atsogoleri anali olakwa.+ Pamenepo ndinawauza kuti: “Nonsenu mukuumiriza abale anu kukupatsani chiwongoladzanja chokwera kwambiri.”+ Kenako ndinaitanitsa msonkhano waukulu chifukwa cha iwowa.+
8 ngati salandira chiwongoladzanja akabwereketsa zinthu,+ ndiponso sakongoza zinthu mwa katapira,*+ ngati sachita zopanda chilungamo,+ ngati amachita chilungamo chenicheni poweruza munthu ndi mnzake,+
13 Iye amakongoza zinthu zake mwa katapira+ ndipo amalandira chiwongoladzanja.+ Ndithudi iye sadzakhala ndi moyo chifukwa wachita zinthu zonyansa zonsezi.+ Adzaphedwa ndithu, ndipo magazi ake adzakhala pamutu pake.+