Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “‘Musamaweruze mopanda chilungamo. Musamakondere munthu wosauka,+ ndiponso musamakondere munthu wolemera.+ Mnzako uzimuweruza mwachilungamo.

  • Levitiko 19:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Usadane ndi m’bale wako mumtima mwako.+ Mnzako um’dzudzule ndithu+ kuti usasenze naye tchimo.

  • 2 Mbiri 19:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno anauza oweruzawo kuti: “Samalani zochita zanu+ chifukwa simukuweruzira munthu koma mukuweruzira Yehova,+ ndipo iye ali nanu pa ntchito yoweruzayi.+

  • 1 Timoteyo 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Anthu amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo,+ uwadzudzule+ pamaso pa onse kuti ena onse akhale ndi mantha.+

  • Tito 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pitiriza kulankhula zimenezi, kulimbikitsa ndi kudzudzula anthu mogwirizana ndi ulamuliro wonse umene wapatsidwa.+ Munthu aliyense asakuderere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena