1 Timoteyo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Usalole kuti munthu aliyense akuderere poona kuti ndiwe wamng’ono.+ M’malomwake, ukhale chitsanzo+ kwa okhulupirika+ m’kalankhulidwe, m’makhalidwe, m’chikondi, m’chikhulupiriro, ndi pa khalidwe loyera.+
12 Usalole kuti munthu aliyense akuderere poona kuti ndiwe wamng’ono.+ M’malomwake, ukhale chitsanzo+ kwa okhulupirika+ m’kalankhulidwe, m’makhalidwe, m’chikondi, m’chikhulupiriro, ndi pa khalidwe loyera.+