1 Akorinto 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho pasadzapezeke munthu womuderera.+ Mudzamuperekeze mu mtendere kuti adzafike kwa ine kunoko, pakuti ineyo ndikumuyembekezera pamodzi ndi abale. Tito 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pitiriza kulankhula zimenezi, kulimbikitsa ndi kudzudzula anthu mogwirizana ndi ulamuliro wonse umene wapatsidwa.+ Munthu aliyense asakuderere.+
11 Choncho pasadzapezeke munthu womuderera.+ Mudzamuperekeze mu mtendere kuti adzafike kwa ine kunoko, pakuti ineyo ndikumuyembekezera pamodzi ndi abale.
15 Pitiriza kulankhula zimenezi, kulimbikitsa ndi kudzudzula anthu mogwirizana ndi ulamuliro wonse umene wapatsidwa.+ Munthu aliyense asakuderere.+