Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 141:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+

      Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+

      Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+

      Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+

  • Miyambo 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Usadzudzule wonyoza kuti angadane nawe.+ Dzudzula munthu wanzeru ndipo adzakukonda.+

  • Mateyu 18:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Komanso, ngati m’bale wako wachimwa, upite kukam’fotokozera cholakwacho panokha iwe ndi iyeyo.+ Ngati wakumvera, ndiye kuti wabweza m’bale wakoyo.+

  • Agalatiya 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma Kefa+ atabwera ku Antiokeya,+ ndinamutsutsa pamasom’pamaso, chifukwa anali wolakwa.+

  • 1 Timoteyo 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Anthu amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo,+ uwadzudzule+ pamaso pa onse kuti ena onse akhale ndi mantha.+

  • Tito 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Umboni umenewu ndi woona. Chifukwa cha zimenezi, pitiriza kuwadzudzula mwamphamvu,+ kuti akhale ndi chikhulupiriro cholimba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena