Levitiko 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Usadane ndi m’bale wako mumtima mwako.+ Mnzako um’dzudzule ndithu+ kuti usasenze naye tchimo. Miyambo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kambirana mlandu wako ndi mnzako,+ ndipo usaulule chinsinsi cha munthu wina,+ Luka 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Samalani ndithu. Ngati m’bale wako wachita tchimo um’dzudzule,+ ndipo akalapa umukhululukire.+