-
Luka 6:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Mosiyana ndi zimenezo, inu pitirizani kukonda adani anu. Pitirizani kuchita zabwino, ndi kukongoza+ popanda chiwongoladzanja, osayembekezera kulandira kalikonse. Mukatero, mphoto yanu idzakhala yaikulu ndipo mudzakhala ana a Wam’mwambamwamba,+ chifukwa iye ndi wachifundo+ kwa osayamika ndi kwa oipa.
-