Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 16:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+

      Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+

  • Salimo 55:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Umutulire Yehova nkhawa zako,+

      Ndipo iye adzakuchirikiza.+

      Sadzalola kuti wolungama agwedezeke.+

  • Miyambo 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Palibe munthu amene angakhazikike chifukwa chochita zoipa,+ koma muzu wa anthu olungama sudzagwedezedwa.+

  • 2 Petulo 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pa chifukwa chimenechi abale, chitani chilichonse chotheka kuti mukhalebe okhulupirika, n’cholinga choti mupitirizebe kukhala pakati pa anthu amene Mulungu wawaitana+ ndi kuwasankha,+ pakuti mukapitiriza kuchita zinthu zimenezi simudzalephera ngakhale pang’ono.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena