Salimo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+ Salimo 37:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma anthu onse ochimwa adzafafanizidwa.+M’tsogolo, anthu oipa adzaphedwa.+
10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+