Aefeso 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 komanso kuti mwa chikhulupiriro chanu, Khristu akhale m’mitima yanu, pamodzi ndi chikondi+ chimene chiyenera kukhala pakati panu, ndiponso kuti muzike mizu+ ndi kukhala okhazikika pamaziko.+ Akolose 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khalanibe ozikika mozama+ mwa iye, ndipo monga mmene munaphunzitsidwira, pitirizani kukula+ pamene mukumuona iye monga maziko anu, ndi kukhazikika m’chikhulupiriro.+ Sefukiranibe ndi chikhulupiriro popereka mapemphero oyamikira.+
17 komanso kuti mwa chikhulupiriro chanu, Khristu akhale m’mitima yanu, pamodzi ndi chikondi+ chimene chiyenera kukhala pakati panu, ndiponso kuti muzike mizu+ ndi kukhala okhazikika pamaziko.+
7 Khalanibe ozikika mozama+ mwa iye, ndipo monga mmene munaphunzitsidwira, pitirizani kukula+ pamene mukumuona iye monga maziko anu, ndi kukhazikika m’chikhulupiriro.+ Sefukiranibe ndi chikhulupiriro popereka mapemphero oyamikira.+