Mateyu 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Chotero aliyense wakumva mawu angawa ndi kuwachita adzafanizidwa ndi munthu wochenjera, amene anamanga nyumba yake pathanthwe.+ Yuda 20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma inu okondedwa, podzilimbitsa+ pamaziko a chikhulupiriro chanu choyera kopambana,+ ndi kupemphera mu mphamvu ya mzimu woyera,+
24 “Chotero aliyense wakumva mawu angawa ndi kuwachita adzafanizidwa ndi munthu wochenjera, amene anamanga nyumba yake pathanthwe.+
20 Koma inu okondedwa, podzilimbitsa+ pamaziko a chikhulupiriro chanu choyera kopambana,+ ndi kupemphera mu mphamvu ya mzimu woyera,+