Salimo 73:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ine ndili ndi inu nthawi zonse.+Mwandigwira dzanja langa lamanja.+ Salimo 121:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova akukuyang’anira.+Yehova ndiye mthunzi wako+ kudzanja lako lamanja.+