Salimo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+ Salimo 73:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ine ndili ndi inu nthawi zonse.+Mwandigwira dzanja langa lamanja.+ Salimo 109:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakuti adzaima kudzanja lamanja la munthu wosauka,+Kuti am’pulumutse kwa omuweruza mopanda chilungamo.
8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+
31 Pakuti adzaima kudzanja lamanja la munthu wosauka,+Kuti am’pulumutse kwa omuweruza mopanda chilungamo.