Salimo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+ Salimo 72:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aweruze osautsika pakati pa anthu,+Apulumutse ana a anthu osauka,Ndipo aphwanye wobera anzake mwachinyengo. Salimo 110:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova amene ali kudzanja lako lamanja+Adzaphwanyaphwanya mafumu pa tsiku la mkwiyo wake.+ Salimo 121:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova akukuyang’anira.+Yehova ndiye mthunzi wako+ kudzanja lako lamanja.+
8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+
4 Aweruze osautsika pakati pa anthu,+Apulumutse ana a anthu osauka,Ndipo aphwanye wobera anzake mwachinyengo.