Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 91:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 91 Aliyense wokhala m’malo otetezeka+ a Wam’mwambamwamba+

      Adzakhala wosungika mumthunzi wa Wamphamvuyonse.+

  • Yesaya 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Akadzatero, malo onse a paphiri la Ziyoni+ ndiponso malo onse a mu Yerusalemu ochitirapo misonkhano, Yehova adzawapangira mtambo ndi utsi kuti ziziwathandiza masana. Adzawapangiranso kuwala kwa moto walawilawi+ kuti kuziwathandiza usiku,+ ndipo pamwamba pa malo onse aulemererowo padzakhala chotchinga.+

  • Yesaya 25:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pakuti inu mwakhala malo achitetezo kwa munthu wonyozeka ndiponso malo achitetezo kwa munthu wosauka m’masautso ake.+ Mwakhala malo ousapo mvula yamkuntho ndi mthunzi+ wobisalirapo kutentha kwa dzuwa. Mwakhala wotero pamene anthu ankhanza akuwomba anzawo ngati mvula yamkuntho yowomba khoma.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena