Salimo 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+ Salimo 121:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova adzakuteteza ku masoka onse.+Iye adzateteza moyo wako.+ Nahumu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo+ pa tsiku la nsautso.+ Amadziwa amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+ Zefaniya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwa iwe ndidzasiyamo anthu ena, odzichepetsa ndi ofatsa,+ ndipo amenewa adzapeza chitetezo m’dzina la Yehova.+
46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+
7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo+ pa tsiku la nsautso.+ Amadziwa amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+
12 Mwa iwe ndidzasiyamo anthu ena, odzichepetsa ndi ofatsa,+ ndipo amenewa adzapeza chitetezo m’dzina la Yehova.+