Salimo 34:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova amawombola moyo wa atumiki ake.+Ndipo palibe aliyense wothawira kwa iye amene adzapezeka wolakwa.+ Salimo 41:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova adzamuteteza ndi kumusunga ali wamoyo.+Adzatchedwa wodala padziko lapansi.+Ndipo Mulungu sangamupereke kwa adani ake.+ Salimo 97:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu okonda Yehova+ danani nacho choipa.+Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawalanditsa m’manja mwa anthu oipa.+ Salimo 145:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova amayang’anira onse omukonda,+Koma oipa onse adzawafafaniza.+
22 Yehova amawombola moyo wa atumiki ake.+Ndipo palibe aliyense wothawira kwa iye amene adzapezeka wolakwa.+
2 Yehova adzamuteteza ndi kumusunga ali wamoyo.+Adzatchedwa wodala padziko lapansi.+Ndipo Mulungu sangamupereke kwa adani ake.+
10 Inu okonda Yehova+ danani nacho choipa.+Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawalanditsa m’manja mwa anthu oipa.+