Salimo 128:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 128 Wodala ndi aliyense woopa Yehova,+Amene amayenda m’njira za Mulungu.+ Mateyu 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Odala ndi anthu achifundo,+ chifukwa adzachitiridwa chifundo. Luka 1:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Chifukwa waona malo otsika a kapolo wake.+ Ndipo taonani! kuyambira tsopano mibadwo yonse idzanditcha wodala.+
48 Chifukwa waona malo otsika a kapolo wake.+ Ndipo taonani! kuyambira tsopano mibadwo yonse idzanditcha wodala.+