Salimo 91:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Palibe tsoka limene lidzakugwera,+Ndipo ngakhale mliri sudzayandikira hema wako.+ Miyambo 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Palibe chopweteka chimene chidzagwere wolungama,+ koma anthu oipa ndi amene tsoka lizidzangowagwera.+
21 Palibe chopweteka chimene chidzagwere wolungama,+ koma anthu oipa ndi amene tsoka lizidzangowagwera.+