Deuteronomo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova adzakuchotserani matenda onse. Ndipo sadzakugwetserani matenda onse oipa a ku Iguputo amene inu mukuwadziwa,+ koma adzawagwetsera pa onse odana nanu. Aheberi 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwa chikhulupiriro, anakhala monga mlendo m’dziko la lonjezo ngati kuti akukhala m’dziko lachilendo.+ Ndipo anali kukhala m’mahema+ pamodzi ndi Isaki+ ndi Yakobo,+ anzake olandira nawo limodzi lonjezolo.+
15 Yehova adzakuchotserani matenda onse. Ndipo sadzakugwetserani matenda onse oipa a ku Iguputo amene inu mukuwadziwa,+ koma adzawagwetsera pa onse odana nanu.
9 Mwa chikhulupiriro, anakhala monga mlendo m’dziko la lonjezo ngati kuti akukhala m’dziko lachilendo.+ Ndipo anali kukhala m’mahema+ pamodzi ndi Isaki+ ndi Yakobo,+ anzake olandira nawo limodzi lonjezolo.+