Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa za ku Iguputo,+ matenda a mudzi,* ziwengo ndi zotupa, ndipo sudzachira matenda amenewa.

  • Deuteronomo 28:60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 60 Adzakubweretsera matenda onse a ku Iguputo amene unachita nawo mantha, ndipo adzakumamatira.+

  • Amosi 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “‘Anthu inu ndinakutumizirani mliri wofanana ndi umene unachitika ku Iguputo.+ Ndinapha anyamata anu ndi lupanga+ ndipo mahatchi anu analandidwa.+ Ndinachititsa fungo lonunkha lotuluka m’misasa yanu kufika kumphuno zanu,+ koma inu simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena