10 “‘Anthu inu ndinakutumizirani mliri wofanana ndi umene unachitika ku Iguputo.+ Ndinapha anyamata anu ndi lupanga+ ndipo mahatchi anu analandidwa.+ Ndinachititsa fungo lonunkha lotuluka m’misasa yanu kufika kumphuno zanu,+ koma inu simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.