Ekisodo 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 dziwa kuti, dzanja la Yehova+ lipha ziweto zanu zonse.+ Mliri waukulu kwambiri ugwera mahatchi,* abulu, ngamila, ng’ombe ndi nkhosa.+ Deuteronomo 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa za ku Iguputo,+ matenda a mudzi,* ziwengo ndi zotupa, ndipo sudzachira matenda amenewa. Deuteronomo 28:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Adzakubweretsera matenda onse a ku Iguputo amene unachita nawo mantha, ndipo adzakumamatira.+ Salimo 78:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mkwiyo wake anaulambulira njira.+Sanawabweze kuwachotsa ku imfa.Ndipo anawapha ndi mliri.+
3 dziwa kuti, dzanja la Yehova+ lipha ziweto zanu zonse.+ Mliri waukulu kwambiri ugwera mahatchi,* abulu, ngamila, ng’ombe ndi nkhosa.+
27 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa za ku Iguputo,+ matenda a mudzi,* ziwengo ndi zotupa, ndipo sudzachira matenda amenewa.