Numeri 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Gwira onse amene akutsogolera anthuwo, uwaphe ndipo mitembo yawo uindandalike padzuwa pamaso pa Yehova.+ Uchite zimenezo kuti mkwiyo wa Yehova umene wayakira Aisiraeli uchoke.”
4 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Gwira onse amene akutsogolera anthuwo, uwaphe ndipo mitembo yawo uindandalike padzuwa pamaso pa Yehova.+ Uchite zimenezo kuti mkwiyo wa Yehova umene wayakira Aisiraeli uchoke.”