2 Samueli 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 mutipatse ana ake aamuna 7,+ ndipo tionetse+ mitembo yawo kwa Yehova mwa kuipachika ku Gibeya,+ kwawo kwa Sauli, munthu amene Yehova+ anamusankha kukhala mfumu.” Pamenepo mfumu inati: “Ndiwapereka m’manja mwanu.”
6 mutipatse ana ake aamuna 7,+ ndipo tionetse+ mitembo yawo kwa Yehova mwa kuipachika ku Gibeya,+ kwawo kwa Sauli, munthu amene Yehova+ anamusankha kukhala mfumu.” Pamenepo mfumu inati: “Ndiwapereka m’manja mwanu.”