1 Samueli 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Samueli ataona Sauli, Yehova anamuuza kuti: “Ameneyu ndiye munthu ndimakuuza uja kuti, ‘Ameneyo ndiye adzalamulire anthu anga.’”+
17 Samueli ataona Sauli, Yehova anamuuza kuti: “Ameneyu ndiye munthu ndimakuuza uja kuti, ‘Ameneyo ndiye adzalamulire anthu anga.’”+