1 Samueli 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Samueli anauza anthu onsewo kuti: “Kodi mwaona amene Yehova wam’sankha,+ kuti palibe aliyense pakati pa anthu onse wofanana naye?” Pamenepo anthu onsewo anayamba kufuula, kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”+ 1 Samueli 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Samueli anati: “Kodi sunali kudziona ngati ndiwe mwana+ utakhala mtsogoleri wa mafuko onse a Isiraeli, pamene Yehova anakudzoza+ kuti ukhale mfumu ya Isiraeli? Machitidwe 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma kuchokera pamenepo anthuwo ananena kuti akufuna mfumu.+ Chotero Mulungu anawapatsa Sauli mwana wa Kisi, munthu wa fuko la Benjamini,+ ndipo anakhala mfumu yawo kwa zaka 40.
24 Ndiyeno Samueli anauza anthu onsewo kuti: “Kodi mwaona amene Yehova wam’sankha,+ kuti palibe aliyense pakati pa anthu onse wofanana naye?” Pamenepo anthu onsewo anayamba kufuula, kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”+
17 Ndiyeno Samueli anati: “Kodi sunali kudziona ngati ndiwe mwana+ utakhala mtsogoleri wa mafuko onse a Isiraeli, pamene Yehova anakudzoza+ kuti ukhale mfumu ya Isiraeli?
21 Koma kuchokera pamenepo anthuwo ananena kuti akufuna mfumu.+ Chotero Mulungu anawapatsa Sauli mwana wa Kisi, munthu wa fuko la Benjamini,+ ndipo anakhala mfumu yawo kwa zaka 40.