Deuteronomo 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 uzidziikira mfumu imene Yehova Mulungu wako adzasankhe.+ Mfumu imene udzadziikire idzachokere pakati pa abale ako. Sudzaloledwa kudziikira mlendo amene si m’bale wako kukhala mfumu. 1 Samueli 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Samueli ataona Sauli, Yehova anamuuza kuti: “Ameneyu ndiye munthu ndimakuuza uja kuti, ‘Ameneyo ndiye adzalamulire anthu anga.’”+
15 uzidziikira mfumu imene Yehova Mulungu wako adzasankhe.+ Mfumu imene udzadziikire idzachokere pakati pa abale ako. Sudzaloledwa kudziikira mlendo amene si m’bale wako kukhala mfumu.
17 Samueli ataona Sauli, Yehova anamuuza kuti: “Ameneyu ndiye munthu ndimakuuza uja kuti, ‘Ameneyo ndiye adzalamulire anthu anga.’”+