1 Samueli 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Samueli ataona Sauli, Yehova anamuuza kuti: “Ameneyu ndiye munthu ndimakuuza uja kuti, ‘Ameneyo ndiye adzalamulire anthu anga.’”+ 1 Samueli 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Samueli anauza anthu onsewo kuti: “Kodi mwaona amene Yehova wam’sankha,+ kuti palibe aliyense pakati pa anthu onse wofanana naye?” Pamenepo anthu onsewo anayamba kufuula, kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”+ 1 Samueli 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anatumadi munthu kukam’tenga. Mnyamatayo anali wamaonekedwe ofiirira,+ mnyamata wa maso okongola, ndiponso wooneka bwino. Pamenepo Yehova anati: “Ndi ameneyu! Nyamuka umudzoze.”+
17 Samueli ataona Sauli, Yehova anamuuza kuti: “Ameneyu ndiye munthu ndimakuuza uja kuti, ‘Ameneyo ndiye adzalamulire anthu anga.’”+
24 Ndiyeno Samueli anauza anthu onsewo kuti: “Kodi mwaona amene Yehova wam’sankha,+ kuti palibe aliyense pakati pa anthu onse wofanana naye?” Pamenepo anthu onsewo anayamba kufuula, kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”+
12 Iye anatumadi munthu kukam’tenga. Mnyamatayo anali wamaonekedwe ofiirira,+ mnyamata wa maso okongola, ndiponso wooneka bwino. Pamenepo Yehova anati: “Ndi ameneyu! Nyamuka umudzoze.”+