Deuteronomo 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Diso lako lisamumvere chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.+ Salimo 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pofunafuna okhetsa magazi,+ iye adzakumbukira ndithu anthu osautsidwa.+Sadzaiwala ndithu kulira kwawo.+
21 Diso lako lisamumvere chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.+
12 Pofunafuna okhetsa magazi,+ iye adzakumbukira ndithu anthu osautsidwa.+Sadzaiwala ndithu kulira kwawo.+