Ekisodo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+ Salimo 72:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Adzawombola miyoyo yawo ku chipsinjo ndi chiwawa,Ndipo adzaona magazi awo kukhala amtengo wapatali.+ Luka 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?
7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+
14 Adzawombola miyoyo yawo ku chipsinjo ndi chiwawa,Ndipo adzaona magazi awo kukhala amtengo wapatali.+
7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?