2 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova sakuchedwa kukwaniritsa lonjezo lake,+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa, koma akuleza nanu mtima, pakuti safuna kuti wina aliyense adzawonongedwe, koma amafuna kuti anthu onse alape.+ Chivumbulutso 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera kufikira liti, Inu Ambuye Wamkulu Koposa,+ woyera ndi woona,+ osaweruza+ ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi+ athu?”
9 Yehova sakuchedwa kukwaniritsa lonjezo lake,+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa, koma akuleza nanu mtima, pakuti safuna kuti wina aliyense adzawonongedwe, koma amafuna kuti anthu onse alape.+
10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera kufikira liti, Inu Ambuye Wamkulu Koposa,+ woyera ndi woona,+ osaweruza+ ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi+ athu?”