1 Samueli 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu,+ ndipo Yehova andibwezerere,+ koma dzanja langali silidzakukhudzani.+ Yesaya 40:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “N’chifukwa chiyani iwe Yakobo, iwe Isiraeli, ukunena kuti: ‘Njira yanga yabisika kwa Yehova,+ ndipo zoti anthu sakundichitira chilungamo Mulungu wanga sakuziona’?+ Yeremiya 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Yehova wa makamu, mumasanthula munthu wolungama.+ Mumaona impso ndi mtima wake.+ Ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango,+ pakuti ine ndakufotokozerani mlandu wanga.+
12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu,+ ndipo Yehova andibwezerere,+ koma dzanja langali silidzakukhudzani.+
27 “N’chifukwa chiyani iwe Yakobo, iwe Isiraeli, ukunena kuti: ‘Njira yanga yabisika kwa Yehova,+ ndipo zoti anthu sakundichitira chilungamo Mulungu wanga sakuziona’?+
12 Inu Yehova wa makamu, mumasanthula munthu wolungama.+ Mumaona impso ndi mtima wake.+ Ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango,+ pakuti ine ndakufotokozerani mlandu wanga.+