Salimo 54:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti anandilanditsa pa mavuto anga onse,+Ndipo diso langa laona adani anga atagonja.+ Salimo 59:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu amene wandisonyeza kukoma mtima kosatha ndidzaonana naye maso ndi maso.+Mulungu adzachititsa kuti ndione adani anga, adaniwo atagonja.+ Yeremiya 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu amene amandizunza achite manyazi+ koma musalole kuti ineyo ndichite manyazi.+ Anthuwo agwidwe ndi mantha aakulu koma musalole kuti ine ndigwidwe ndi mantha aakulu. Agwetsereni tsoka+ ndipo muwaphwanye kuwirikiza kawiri.+
10 Mulungu amene wandisonyeza kukoma mtima kosatha ndidzaonana naye maso ndi maso.+Mulungu adzachititsa kuti ndione adani anga, adaniwo atagonja.+
18 Anthu amene amandizunza achite manyazi+ koma musalole kuti ineyo ndichite manyazi.+ Anthuwo agwidwe ndi mantha aakulu koma musalole kuti ine ndigwidwe ndi mantha aakulu. Agwetsereni tsoka+ ndipo muwaphwanye kuwirikiza kawiri.+