Salimo 54:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti anandilanditsa pa mavuto anga onse,+Ndipo diso langa laona adani anga atagonja.+ Salimo 92:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Diso langa lidzayang’ana adani anga atagonja,+Makutu anga adzamva za anthu ondiukira, anthu ochita zoipa.
11 Diso langa lidzayang’ana adani anga atagonja,+Makutu anga adzamva za anthu ondiukira, anthu ochita zoipa.