2 Samueli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma Davide anayankha Rekabu ndi m’bale wake Bana, ana a Rimoni Mbeeroti kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ amene anawombola+ moyo wanga+ m’masautso anga onse,+ Salimo 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Masoka a munthu wolungama ndi ochuluka,+Koma Yehova amamupulumutsa ku masoka onsewo.+ Salimo 37:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+ 2 Timoteyo 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ambuye adzandipulumutsa ku choipa chilichonse+ ndipo adzandisungira ufumu wake wakumwamba.+ Iye apatsidwe ulemerero mpaka muyaya. Ame.
9 Koma Davide anayankha Rekabu ndi m’bale wake Bana, ana a Rimoni Mbeeroti kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ amene anawombola+ moyo wanga+ m’masautso anga onse,+
39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+
18 Ambuye adzandipulumutsa ku choipa chilichonse+ ndipo adzandisungira ufumu wake wakumwamba.+ Iye apatsidwe ulemerero mpaka muyaya. Ame.