1 Samueli 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu,+ ndipo Yehova andibwezerere,+ koma dzanja langali silidzakukhudzani.+ 1 Samueli 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Udalitsike mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu ndipo udzapambana ndithu.”+ Pamenepo Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+ 2 Samueli 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Natani anauza Davide kuti: “Munthu ameneyo ndiwe! Choncho Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ine ndinakudzoza+ iwe kuti ukhale mfumu ya Isiraeli ndipo ndinakupulumutsa+ m’manja mwa Sauli.
12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu,+ ndipo Yehova andibwezerere,+ koma dzanja langali silidzakukhudzani.+
25 Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Udalitsike mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu ndipo udzapambana ndithu.”+ Pamenepo Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+
7 Pamenepo Natani anauza Davide kuti: “Munthu ameneyo ndiwe! Choncho Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ine ndinakudzoza+ iwe kuti ukhale mfumu ya Isiraeli ndipo ndinakupulumutsa+ m’manja mwa Sauli.