Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ndiyeno Yehova+ atamaliza kulankhula ndi Abulahamu, ananyamuka n’kumapita, ndipo Abulahamu anabwerera kunyumba kwake.

  • Numeri 24:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Tsopano Balamu ananyamuka kumabwerera kwawo.+ Nayenso Balaki ananyamuka kulowera njira yake.

  • 1 Samueli 24:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Zitatero, Davide analumbirira Sauli. Kenako Sauliyo anapita kwawo,+ koma Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anapita kumalo ovuta kufikako.+

  • 1 Samueli 27:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Patapita nthawi, uthenga unafika kwa Sauli wonena kuti Davide anathawira ku Gati. Atamva zimenezo sanapitenso kukam’sakasaka.+

  • 2 Samueli 19:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Tsopano anthu onse anayamba kuwoloka Yorodano, ndipo mfumu nayonso inawoloka. Koma mfumu inapsompsona+ Barizilai ndi kumudalitsa,+ kenako Barizilai anabwerera kwawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena