1 Samueli 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Davide anayamba kukhala m’chipululu, m’malo ovuta kufikako. Iye anapitiriza kukhala m’dera lamapiri m’chipululu cha Zifi,+ ndipo Sauli anali kumufunafuna nthawi zonse,+ koma Mulungu sanam’pereke m’manja mwake.+ 1 Samueli 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Udalitsike mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu ndipo udzapambana ndithu.”+ Pamenepo Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+
14 Tsopano Davide anayamba kukhala m’chipululu, m’malo ovuta kufikako. Iye anapitiriza kukhala m’dera lamapiri m’chipululu cha Zifi,+ ndipo Sauli anali kumufunafuna nthawi zonse,+ koma Mulungu sanam’pereke m’manja mwake.+
25 Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Udalitsike mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu ndipo udzapambana ndithu.”+ Pamenepo Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+