Genesis 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo, amunawo anatembenuka kulowera ku Sodomu, koma Yehova+ anatsala ataima ndi Abulahamu.+